Ekisodo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+
17 “Usalakelake nyumba ya mnzako. Usalakelake mkazi wa mnzako,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake, bulu wake, kapena chilichonse cha mnzako.”+