Luka 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho anamuitana ndi kumuuza kuti, ‘Ndamva zoipa zimene ukuchita. Pita ukalembe lipoti la mmene wagwirira ntchito yoyang’anira nyumba ino udzandipatse,+ pakuti supitiriza kuyendetsa ntchito za panyumba pano.’ 1 Akorinto 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndikachita zimenezi mwaufulu,+ ndili ndi mphoto.+ Koma ndikachita motsutsana ndi kufuna kwanga, sindingachitire mwina, ndinebe woyang’anira mogwirizana ndi udindo+ umene unaikidwa m’manja mwanga. Aefeso 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndithudi munamva kuti ndinaikidwa kukhala woyang’anira+ kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kuti ndikuthandizeni,
2 Choncho anamuitana ndi kumuuza kuti, ‘Ndamva zoipa zimene ukuchita. Pita ukalembe lipoti la mmene wagwirira ntchito yoyang’anira nyumba ino udzandipatse,+ pakuti supitiriza kuyendetsa ntchito za panyumba pano.’
17 Ndikachita zimenezi mwaufulu,+ ndili ndi mphoto.+ Koma ndikachita motsutsana ndi kufuna kwanga, sindingachitire mwina, ndinebe woyang’anira mogwirizana ndi udindo+ umene unaikidwa m’manja mwanga.
2 Ndithudi munamva kuti ndinaikidwa kukhala woyang’anira+ kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kuti ndikuthandizeni,