Machitidwe 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Ayuda+ anauza zoipa amayi otchuka amene anali opembedza Mulungu, komanso amuna olemekezeka a mumzindawo. Chotero iwowa anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa,+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.
50 Koma Ayuda+ anauza zoipa amayi otchuka amene anali opembedza Mulungu, komanso amuna olemekezeka a mumzindawo. Chotero iwowa anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa,+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.