1 Timoteyo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Paja nditatsala pang’ono kupita ku Makedoniya, ndinakulimbikitsa kuti ukhalebe ku Efeso.+ Ndikukulimbikitsanso kuti ukhalebe komweko, uletse+ anthu ena ake kuti asaphunzitse chiphunzitso chosiyana ndi chathu,+ 1 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+ 1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+
3 Paja nditatsala pang’ono kupita ku Makedoniya, ndinakulimbikitsa kuti ukhalebe ku Efeso.+ Ndikukulimbikitsanso kuti ukhalebe komweko, uletse+ anthu ena ake kuti asaphunzitse chiphunzitso chosiyana ndi chathu,+
10 adama,+ amuna ogonana ndi amuna anzawo, oba anthu, onama, olumbira monama,+ ndiponso ochita china chilichonse chosagwirizana+ ndi chiphunzitso cholondola.+
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+