1 Timoteyo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera iwe Timoteyo,+ mwana wanga weniweni+ m’chikhulupiriro: Kukoma mtima kwakukulu, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu, zikhale nawe.+
2 ndikulembera iwe Timoteyo,+ mwana wanga weniweni+ m’chikhulupiriro: Kukoma mtima kwakukulu, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu, zikhale nawe.+