Aefeso 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika. 1 Timoteyo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ndikufuna kuti kulikonse amuna apitirize kupemphera, kukweza m’mwamba manja awo oyera+ popanda kukwiyirana+ ndi kutsutsana.+
24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.
8 Choncho, ndikufuna kuti kulikonse amuna apitirize kupemphera, kukweza m’mwamba manja awo oyera+ popanda kukwiyirana+ ndi kutsutsana.+