Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Timoteyo 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nthawi zonse uzisamala ndi zimene umachita+ komanso zimene umaphunzitsa.+ Pitiriza kuchita zimenezi, chifukwa ukatero udzadzipulumutsa wekha komanso anthu okumvera.+

  • 1 Timoteyo 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ngati munthu akuphunzitsa chiphunzitso china,+ ndipo sakuvomereza mawu olondola,+ mawu a Ambuye wathu Yesu Khristu, ndiponso sakuvomereza chiphunzitso chogwirizana ndi kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+

  • Yakobo 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu,+ podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chachikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena