1 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+
11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+