Aefeso 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero ine, amene ndili m’ndende+ chifukwa cha Ambuye, ndikukuchondererani kuti muziyenda moyenera+ kuitana kumene munaitanidwa nako.+
4 Chotero ine, amene ndili m’ndende+ chifukwa cha Ambuye, ndikukuchondererani kuti muziyenda moyenera+ kuitana kumene munaitanidwa nako.+