2 Akorinto 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sindikukulamulani,+ koma ndikulankhula izi chifukwa cha khama limene ena asonyeza, kutinso ndione ngati chikondi chanu chilidi chenicheni. Agalatiya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zoonadi abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu,+ musayese ngakhale pang’ono kugwiritsa ntchito ufulu umenewu polimbikitsira zilakolako za thupi,+ koma tumikiranani mwachikondi.+
8 Sindikukulamulani,+ koma ndikulankhula izi chifukwa cha khama limene ena asonyeza, kutinso ndione ngati chikondi chanu chilidi chenicheni.
13 Zoonadi abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu,+ musayese ngakhale pang’ono kugwiritsa ntchito ufulu umenewu polimbikitsira zilakolako za thupi,+ koma tumikiranani mwachikondi.+