Aefeso 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chifukwa chake inenso, kuyambira pamene ndinamva za chikhulupiriro chimene muli nacho mwa Ambuye Yesu ndi mmene mumachisonyezera m’zochita zanu ndi oyera onse,+ Akolose 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Timatero chifukwa tinamva za chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu, ndi chikondi chanu pa oyera onse,+
15 Ndiye chifukwa chake inenso, kuyambira pamene ndinamva za chikhulupiriro chimene muli nacho mwa Ambuye Yesu ndi mmene mumachisonyezera m’zochita zanu ndi oyera onse,+
4 Timatero chifukwa tinamva za chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu, ndi chikondi chanu pa oyera onse,+