Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Anawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+