2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu. Maliko 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+ Luka 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+ 2 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+
14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu.
11 Pamenepo panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+
35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+
17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+