Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ 2 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+