Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.

  • Genesis 17:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzakupatsa ana ambiri zedi, ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu ndi mafumu.+

  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+

  • Aroma 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+

  • Agalatiya 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano, malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu+ ndi kwa mbewu yake.+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbewu zako,” ngati kuti mbewuzo n’zambiri, koma amanena za mbewu imodzi+ kuti: “Kwa mbewu yako,”+ amene ndi Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena