Salimo 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sindikukudzudzulani chifukwa cha nsembe zanu,+Kapena chifukwa cha nsembe zanu zopsereza zathunthu zimene mumapereka kwa ine nthawi zonse.+ Amosi 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mukapereka nsembe zathunthu zopsereza,+ ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo zoperekedwa ngati mphatso,+ ndipo sindidzayang’ana nsembe zanu zachiyanjano zanyama zonenepa.+
8 Sindikukudzudzulani chifukwa cha nsembe zanu,+Kapena chifukwa cha nsembe zanu zopsereza zathunthu zimene mumapereka kwa ine nthawi zonse.+
22 Inu mukapereka nsembe zathunthu zopsereza,+ ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo zoperekedwa ngati mphatso,+ ndipo sindidzayang’ana nsembe zanu zachiyanjano zanyama zonenepa.+