Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.

  • 1 Akorinto 15:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti Mulungu “anaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Koma pamene akunena kuti ‘waika zinthu zonse pansi pake,’+ n’zodziwikiratu kuti sakuphatikizapo amene anaika zinthu zonsezo pansi pa iye.+

  • Aefeso 1:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi a iyeyo,+ ndipo anamuika mutu wa zinthu zonse+ chifukwa cha mpingo,

  • Afilipi 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iyeyo adzakonzanso thupi lathu lonyozekali+ kuti lifanane ndi thupi lake laulemerero.+ Adzatero malinga ndi mphamvu+ imene ali nayo, yotha kugonjetsera+ ngakhale zinthu zonse kwa iye mwini.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena