Mateyu 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kulalikira ndi kunena kuti: “Lapani+ anthu inu, pakuti ufumu+ wakumwamba wayandikira.” Mateyu 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+ Afilipi 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ife, ndife nzika+ zakumwamba,+ kumenekonso tikuyembekezera mwachidwi+ mpulumutsi, Ambuye Yesu Khristu.+
17 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kulalikira ndi kunena kuti: “Lapani+ anthu inu, pakuti ufumu+ wakumwamba wayandikira.”
34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+
20 Koma ife, ndife nzika+ zakumwamba,+ kumenekonso tikuyembekezera mwachidwi+ mpulumutsi, Ambuye Yesu Khristu.+