-
Ekisodo 1:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 kuti: “Pamene mukuthandiza amayi achiheberi kubereka, mukaona kuti mwana akubadwayo ndi wamwamuna muzimupha, koma ngati ndi wamkazi muzimusiya wamoyo.”
-