Ekisodo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anawauza kuti: “Mukamathandiza amayi a Chiheberi kubereka+ ndipo mwaona kuti mwana amene akubadwayo ndi wamwamuna muzimupha, koma ngati ndi wamkazi muzimusiya wamoyo.”
16 Iye anawauza kuti: “Mukamathandiza amayi a Chiheberi kubereka+ ndipo mwaona kuti mwana amene akubadwayo ndi wamwamuna muzimupha, koma ngati ndi wamkazi muzimusiya wamoyo.”