Yobu 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iweyo walangiza anthu ambiri,+Ndipo manja ofooka unali kuwalimbitsa.+ Yesaya 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa,+ ndipo wofooka amam’patsa nyonga zochuluka.+ Luka 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndakupempherera+ iwe kuti chikhulupiriro chako chisathe. Chotero iwenso, ukabwerera, ukalimbikitse+ abale ako.”
32 Koma ine ndakupempherera+ iwe kuti chikhulupiriro chako chisathe. Chotero iwenso, ukabwerera, ukalimbikitse+ abale ako.”