Luka 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Samalani ndithu. Ngati m’bale wako wachita tchimo um’dzudzule,+ ndipo akalapa umukhululukire.+