Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Agalatiya 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Abale, ngati munthu wapatuka n’kuyamba kulowera njira yolakwika+ mosazindikira, inu oyenerera mwauzimu,+ yesani kumuthandiza munthu woteroyo ndi mzimu wofatsa.+ Pamene mukutero, aliyense wa inu asamale,+ kuopera kuti iyenso angayesedwe.+

  • Yakobo 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa wodwalayo,+ ndipo Yehova adzamulimbitsa.+ Ndiponso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.+

  • Yuda 23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Apulumutseni+ mwa kuwakwatula pamoto.+ Pitirizaninso kuchitira chifundo ena onse, koma ndi mantha. Iwo aipitsa zovala zawo zamkati ndi ntchito za thupi. Choncho pamene mukuwachitira chifundo, mutalikirane kwambiri ndi zovala zawo zoipitsidwazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena