Aheberi 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti anali kuyembekezera mzinda+ wokhala ndi maziko enieni, mzinda umene Mulungu ndiye anaumanga ndi kuupanga.+ Aheberi 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti pamene tili pano, tilibe mzinda wokhazikika,+ koma ndi mtima wonse tikufunitsitsa mzinda umene ukubwerawo.+
10 Pakuti anali kuyembekezera mzinda+ wokhala ndi maziko enieni, mzinda umene Mulungu ndiye anaumanga ndi kuupanga.+
14 Pakuti pamene tili pano, tilibe mzinda wokhazikika,+ koma ndi mtima wonse tikufunitsitsa mzinda umene ukubwerawo.+