Yohane 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Atate wanu Abulahamu anali wosangalala poyembekezera kuona tsiku langa,+ ndipo analiona moti anakondwera.”+ Aheberi 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti pamene tili pano, tilibe mzinda wokhazikika,+ koma ndi mtima wonse tikufunitsitsa mzinda umene ukubwerawo.+ Chivumbulutso 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+
56 Atate wanu Abulahamu anali wosangalala poyembekezera kuona tsiku langa,+ ndipo analiona moti anakondwera.”+
14 Pakuti pamene tili pano, tilibe mzinda wokhazikika,+ koma ndi mtima wonse tikufunitsitsa mzinda umene ukubwerawo.+
2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+