Yeremiya 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova. Machitidwe 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli, mwa kumuchitira utumiki wopatulika mosalekeza usana ndi usiku.+ Chotero Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+
31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova.
7 Ndipo mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli, mwa kumuchitira utumiki wopatulika mosalekeza usana ndi usiku.+ Chotero Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+