20 Iye akudya phulusa.+ Mtima wake umene wanyengedwa wamusocheretsa.+ Iye sakupulumutsa moyo wake kapena kunena kuti: “Kodi chinthu chimene chili m’dzanja langa lamanjachi si chonyenga?”+
16 Pakuti chilichonse cha m’dziko,+ monga chilakolako cha thupi,+ chilakolako cha maso+ ndi kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake,+ sizichokera kwa Atate, koma kudziko.+