Machitidwe 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawiyo mu Yerusalemu munali kukhala Ayuda ena,+ anthu oopa Mulungu,+ ochokera mu mtundu uliwonse mwa mitundu ya pansi pa thambo. Machitidwe 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha. 1 Petulo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Petulo mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera inu osankhidwa ndi Mulungu,+ amene muli alendo osakhalitsa,+ amene mwamwazikana+ ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya,+ Asia, ndi ku Bituniya.
5 Pa nthawiyo mu Yerusalemu munali kukhala Ayuda ena,+ anthu oopa Mulungu,+ ochokera mu mtundu uliwonse mwa mitundu ya pansi pa thambo.
8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha.
1 Ine Petulo mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera inu osankhidwa ndi Mulungu,+ amene muli alendo osakhalitsa,+ amene mwamwazikana+ ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya,+ Asia, ndi ku Bituniya.