Genesis 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako iwo anafika pamalo amene Mulungu woona anamuuza Abulahamu. Atafika pamalowo, iye anamanga guwa lansembe+ n’kuyala nkhuni zija paguwapo. Atatero, anamanga Isaki mwana wakeyo manja ndi miyendo, n’kumugoneka paguwapo, pamwamba pa nkhuni.+ Genesis 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno mngeloyo anapitiriza kulankhula kuti: “Usatambasulire dzanja lako mwanayo ndipo usam’chite kanthu kena kalikonse.+ Tsopano ndadziwa kuti ndiwe woopa Mulungu, pakuti sunakane kupereka kwa ine mwana wako mmodzi yekhayo.”+
9 Kenako iwo anafika pamalo amene Mulungu woona anamuuza Abulahamu. Atafika pamalowo, iye anamanga guwa lansembe+ n’kuyala nkhuni zija paguwapo. Atatero, anamanga Isaki mwana wakeyo manja ndi miyendo, n’kumugoneka paguwapo, pamwamba pa nkhuni.+
12 Ndiyeno mngeloyo anapitiriza kulankhula kuti: “Usatambasulire dzanja lako mwanayo ndipo usam’chite kanthu kena kalikonse.+ Tsopano ndadziwa kuti ndiwe woopa Mulungu, pakuti sunakane kupereka kwa ine mwana wako mmodzi yekhayo.”+