Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 26:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+

  • Aheberi 11:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma anadziwa kuti Mulungu ali ndi mphamvu zomuukitsa kwa akufa.+ Ndipo iye anamulandiradi kuchokera kwa akufa m’njira ya fanizo.+

  • Yakobo 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kodi Abulahamu atate wathu+ sanayesedwe wolungama chifukwa cha ntchito zake, atapereka Isaki mwana wake nsembe paguwa?+

  • 1 Yohane 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chikondi chimenechi chikutanthauza kuti ife sitinakonde Mulungu, koma iye ndi amene anatikonda ndi kutumiza Mwana wake monga nsembe+ yophimba+ machimo athu.+

  • 1 Yohane 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena