Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musabwezere choipa pa choipa.+ Chitani zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino. 2 Akorinto 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti “timasamalira zinthu zonse moona mtima, osati pamaso pa Yehova pokha ayi, komanso pamaso pa anthu.”+ 1 Timoteyo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.
21 Pakuti “timasamalira zinthu zonse moona mtima, osati pamaso pa Yehova pokha ayi, komanso pamaso pa anthu.”+
7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.