Aroma 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa,+ osati ngati ukuchita zabwino. Choncho kodi ukufuna kuti usamachite mantha ndi olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda.
3 Pakuti olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa,+ osati ngati ukuchita zabwino. Choncho kodi ukufuna kuti usamachite mantha ndi olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda.