Ezekieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+ Malaki 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Taonani! Ine nditumiza mthenga wanga+ ndipo iye adzandikonzera njira.+ Mwadzidzidzi, Ambuye woona, amene anthu inu mukumufunafuna, adzabwera kukachisi+ Wake.+ Adzabwera ndi mthenga+ wa pangano+ amene mukumuyembekezera mosangalala.+ Iye adzabwera ndithu,” watero Yehova wa makamu.+
6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+
3 “Taonani! Ine nditumiza mthenga wanga+ ndipo iye adzandikonzera njira.+ Mwadzidzidzi, Ambuye woona, amene anthu inu mukumufunafuna, adzabwera kukachisi+ Wake.+ Adzabwera ndi mthenga+ wa pangano+ amene mukumuyembekezera mosangalala.+ Iye adzabwera ndithu,” watero Yehova wa makamu.+