22 Wotenga malo amenewa akhale munthu amene wakhala akusonkhana nafe kuyambira pamene Yesu anabatizidwa+ ndi Yohane, kudzafika tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba kuchoka pakati pathu.+ Mmodzi wa amuna amenewa, akhale mboni ya kuuka kwake pamodzi ndi ife.”+