Luka 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 kuti mukadye+ ndi kumwa patebulo langa mu ufumu wanga,+ ndipo mukakhala m’mipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli. Yohane 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’nyumba ya Atate wanga muli malo ambiri okhalamo.+ Akanapanda kukhalamo, ndikanakuuzani, chifukwa ndikupita kukakukonzerani malo.+ Agalatiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+
30 kuti mukadye+ ndi kumwa patebulo langa mu ufumu wanga,+ ndipo mukakhala m’mipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.
2 M’nyumba ya Atate wanga muli malo ambiri okhalamo.+ Akanapanda kukhalamo, ndikanakuuzani, chifukwa ndikupita kukakukonzerani malo.+
29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+