1 Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene ali wogwirizana+ ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Aliyense amene amachita tchimo ndiye kuti sanamuone kapena kumudziwa.+ 1 Yohane 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene ali mwana wa Mulungu sapitiriza kuchita tchimo,+ chifukwa mbewu ya Mulungu yopatsa moyo imakhalabe mwa munthu ameneyo, ndipo sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, chifukwa ndi mwana wa Mulungu.+ 1 Yohane 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ife tikudziwa ndipo tikukhulupirira za chikondi+ chimene Mulungu ali nacho kwa ife. Mulungu ndiye chikondi,+ ndipo munthu amene amapitiriza kusonyeza chikondi,+ amakhalabe wogwirizana ndi Mulungu ndiponso Mulungu amakhala wogwirizana+ naye.
6 Aliyense amene ali wogwirizana+ ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Aliyense amene amachita tchimo ndiye kuti sanamuone kapena kumudziwa.+
9 Aliyense amene ali mwana wa Mulungu sapitiriza kuchita tchimo,+ chifukwa mbewu ya Mulungu yopatsa moyo imakhalabe mwa munthu ameneyo, ndipo sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, chifukwa ndi mwana wa Mulungu.+
16 Ife tikudziwa ndipo tikukhulupirira za chikondi+ chimene Mulungu ali nacho kwa ife. Mulungu ndiye chikondi,+ ndipo munthu amene amapitiriza kusonyeza chikondi,+ amakhalabe wogwirizana ndi Mulungu ndiponso Mulungu amakhala wogwirizana+ naye.