Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 33:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndipo anawonjezera kuti: “Sungathe kuona nkhope yanga, chifukwa palibe munthu angandione n’kukhalabe ndi moyo.”+

  • Yohane 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+

  • Yohane 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+

  • Yohane 5:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Komanso Atate amene anandituma andichitira umboni.+ Inu simunamvepo mawu ake nthawi ina iliyonse, kapena kuona thupi lake.+

  • Yohane 6:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Sikuti alipo munthu amene anaonapo Atate ayi,+ kupatulapo yekhayo amene anachokera kwa Mulungu, ameneyu anaona Atate.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena