Yohane 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma munthu akayenda usiku,+ amapunthwa pa chinachake chifukwa mwa iye mulibe kuwala.” 2 Petulo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene alibe zinthu zimenezi ndi wakhungu, wotseka maso ake kuti asaone kuwala,+ ndipo waiwala+ kuti anayeretsedwa+ ku machimo ake akale. 1 Yohane 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+
9 Munthu amene alibe zinthu zimenezi ndi wakhungu, wotseka maso ake kuti asaone kuwala,+ ndipo waiwala+ kuti anayeretsedwa+ ku machimo ake akale.
20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+