Numeri 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+ 1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo. Afilipi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzichita zinthu zonse popanda kung’ung’udza+ ndi kutsutsana,+
27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+
10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo.