Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+ 1 Timoteyo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene ukundiyembekezera, pitiriza kukhala wodzipereka powerenga+ pamaso pa anthu,+ powadandaulira, ndi powaphunzitsa.
2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+
13 Pamene ukundiyembekezera, pitiriza kukhala wodzipereka powerenga+ pamaso pa anthu,+ powadandaulira, ndi powaphunzitsa.