Chivumbulutso 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+
7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+