Levitiko 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+ Chivumbulutso 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ndinaona chizindikiro china+ kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Ndicho angelo 7+ okhala ndi miliri 7.+ Imeneyi ndiyo yomaliza, chifukwa ndiyo ikumalizitsa+ mkwiyo+ wa Mulungu.
21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+
15 Ndipo ndinaona chizindikiro china+ kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Ndicho angelo 7+ okhala ndi miliri 7.+ Imeneyi ndiyo yomaliza, chifukwa ndiyo ikumalizitsa+ mkwiyo+ wa Mulungu.