Chivumbulutso 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Odala ndiwo amene achapa mikanjo+ yawo, kuti akhale ndi ufulu wa kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndiponso kuti akalowe mumzindawo kudzera pazipata zake.+
14 Odala ndiwo amene achapa mikanjo+ yawo, kuti akhale ndi ufulu wa kudya zipatso za m’mitengo ya moyo,+ ndiponso kuti akalowe mumzindawo kudzera pazipata zake.+