Danieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma oyera+ a Wamkulukulu+ adzalandira ufumu ndipo adzatenga ufumuwo+ mpaka kalekale, ku nthawi zosatha.’ Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo. Chivumbulutso 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nditayang’ana, ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Limodzi naye panali enanso 144,000+ olembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pamphumi pawo.
18 Koma oyera+ a Wamkulukulu+ adzalandira ufumu ndipo adzatenga ufumuwo+ mpaka kalekale, ku nthawi zosatha.’
21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.
14 Nditayang’ana, ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Limodzi naye panali enanso 144,000+ olembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pamphumi pawo.