2 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu amaphunzitsa,+ ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye amaphunzitsa, amavomerezedwa ndi Atate ndiponso Mwana.+ Chivumbulutso 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ndinaona chizindikiro china+ kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Ndicho angelo 7+ okhala ndi miliri 7.+ Imeneyi ndiyo yomaliza, chifukwa ndiyo ikumalizitsa+ mkwiyo+ wa Mulungu.
9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu amaphunzitsa,+ ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye amaphunzitsa, amavomerezedwa ndi Atate ndiponso Mwana.+
15 Ndipo ndinaona chizindikiro china+ kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Ndicho angelo 7+ okhala ndi miliri 7.+ Imeneyi ndiyo yomaliza, chifukwa ndiyo ikumalizitsa+ mkwiyo+ wa Mulungu.