Chivumbulutso 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndikubwera mofulumira.+ Gwirabe mwamphamvu chimene uli nacho,+ kuti wina asakulande mphoto* yako.+ Chivumbulutso 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo taonani! Ndikubwera mofulumira.+ Wodala ndi aliyense wosunga mawu a ulosi a mumpukutu uwu.”+
11 Ndikubwera mofulumira.+ Gwirabe mwamphamvu chimene uli nacho,+ kuti wina asakulande mphoto* yako.+