Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, ndinu odala mukamazichita.+ Chivumbulutso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wodala+ ndi munthu amene amawerenga mokweza,+ ndiponso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu,+ komanso amene akusunga zolembedwamo,+ pakuti nthawi yoikidwiratu ili pafupi.+
3 Wodala+ ndi munthu amene amawerenga mokweza,+ ndiponso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu,+ komanso amene akusunga zolembedwamo,+ pakuti nthawi yoikidwiratu ili pafupi.+