Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mulungu anamuyankha Mose kuti: “NDIDZAKHALA AMENE NDIDZAFUNE KUKHALA.”+ Ndiyeno anawonjezera kuti: “Ana a Isiraeli ukawauze kuti, ‘NDIDZAKHALA AMENE NDIDZAFUNE KUKHALA ndiye wandituma kwa inu.’”+

  • Chivumbulutso 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,+ Wamphamvuyonse.”+

  • Chivumbulutso 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Zamoyo zinayizo,+ chilichonse chinali ndi mapiko 6.+ Zinali ndi maso thupi lonse ngakhalenso kunsi kwa mapiko.+ Zamoyo zimenezi sizinali kupuma usana ndi usiku. Zinali kunena kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova+ Mulungu, Wamphamvuyonse,+ amene analipo, amene alipo,+ ndi amene akubwera.”

  • Chivumbulutso 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena