Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+ 2 Akorinto 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa Amakedoniya. Ndikumawauza kuti, “Abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano,”+ ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa ambiri a iwo.
9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+
2 Pakuti ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa Amakedoniya. Ndikumawauza kuti, “Abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano,”+ ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa ambiri a iwo.