Miyambo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthumwi yokhulupirika kwa anthu amene aituma ili ngati kuzizira kwa chipale chofewa+ pa tsiku lokolola, chifukwa imatsitsimula moyo wa ambuye ake.+ Miyambo 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhani yabwino yochokera kudziko lakutali+ ili ngati madzi ozizira kwa munthu wotopa.+
13 Nthumwi yokhulupirika kwa anthu amene aituma ili ngati kuzizira kwa chipale chofewa+ pa tsiku lokolola, chifukwa imatsitsimula moyo wa ambuye ake.+